Zofunika kuziwa pa azphunzitsi athu.
Aziphunzitsi omwe aphunzitsa pa sukulu ndi nzika zam`maiko omwe apezeka. Nthawi zina zapadera timalowetsa nchit azphunzitso akhala pomwepo ngati ali ndi nazo zofunikira monga mapepala a chitsimikizo ca maphunziro apa mwamba . Aziphuniztsi achilankhulidwe chachiportuegese achokera ku Portugal, Angola, Mozambique, Brazil, Sao, Tome Aziphunzitsi a chilankhulidwe chachi spanishi ndi nzika za ku Spain, Spanish amerika (chapakti ndi kumwera kwa Amerika ndinso zisumbu za ku karibean)Zinenero zina ndizaku malo awa Aragonese, Astrian, Andualusianndi Castilian.
Achilankhol chachi french achokera kut France, Ivory coast, French Canada, Zimbabwe, Togo, Benin, A chilankhulo chahci chingerezi achokera ku Ghana, U K, USA Cananda, Australia, South Africa Nigeria.
A chilankhulo chahci Japanese achokera ku Japan. Sukulu likuitana nzika zam`maiko oterewa
A chilankhulo ca ku Itali achokera ku dziko la Italy Pa nthawi imodzi-modzi sukulu likuitana nzika zatere.
A chilankhbo chachi Dutch achokera ku Nerthalans ndi Flemish Zone
A chilankhulo ca Arabic tiri nao okwanila khumi ndi atatu(13) omwe pali pano ali kuyembekeza kuyamba nchito.
A chilsankhulo chachi Hausa achokera ku Ghana ndi nigeria, Achilankhulo chachi Swahili achokera ku Kenya, Tanzania, Tanganyika ndi Zanzibar.
Azilankhulo za Twi, Fante, Ga Dangme achokera ku Ghana.
Achilankhulo chachi chinese achokera ku China.
Achilankhulo chahci Russian achokera ku Rissia.
A chilankhulo chahci Denish: Sukulu likufuna-funa ena azphunzitsi achilankhuochi.
ChiFinish: sukulu lifunabe ena aziphunzitsi achilankhulochi.
Ch Swedish: sukulu likufuna ena aziphunzitso achilankhulochi.
Chi Norweigian: Sukulu likali kufunabe ena aziphunzitsi achilankhulochi.
Wroclaw buiroat active scholl .com.pl, solodaat yahoo.com, tel/fax 341-91-10,tel: 341-91-54 mobile: 6o7986645.
|