|
Zokhuzana nazo kapena kuti zopamaluma nazo.
Timakhuzana ndi chigao ca zamaphunziro muziko la Portugal, Italy, Ecuador, Ghana, Cananda, Ziko La USA, Britain Australia, Brazil, Angola Zimbabwe, Togo Benin, Ivory Coast, France, Swtserland Holand, Nerthaland, Finland, Denm,ark, Sweden, norway, Germany ndi Belgium pofuna kusonyeza kiziwika kwathu, kuziwa ubwino wa nmaskulu ao ndi maskulu akulu-akulua apa mwamba ndi zofunikira maiko osiyana-siyana.
Njira zimenezi zimathithasndiza kukhazikitsa zabwino za sukulu la changu yomwe ili pamwamba koposa masukulu ena m`maiko osiyana-siyana. Nfundo imeneyi ndi zochita zathu zimatithandiza m`mene ochita maphunziro omwe atsiriza maphunziro ao kuchokera pa sukulu lathu kukhala okwima kuposa aja omwe amaliza maphunziro ao m`masukulu ena amaiko amenewa. Timatenga dongosolo la maphunziro m`masukulu omwe alimo, zonse zomwe agwilitsa nchito pomwe akuchita maphunziro ao chaka ndi chaka, mitundu ya zomwe agwilitsa nchito akalibe kuti alandire mapepala achitsimikizo chokwanitsa maphunziro akuya m`masukulu omwe tachula pamwambapa ndinso kuona pa kukwima kwa mayeso omwe analemba. Timayesanso kuchita chotheka kuona m`mabuku a ndonda kotero kuti tione omwe anakhala opambana m`maphunziro ndi zomwe anaphata kulingana ndi maphunziro omwe analandira.
|